Lamentations 4:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidachitika chifukwa cha machimo a aneneri ake ndi ntchito zoipa za ansembe ake, amene ankakhetsa magazi a anthu osalakwa m'malinga amumzindamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndicho chifukwa cha machimo a aneneri ndi mphulupulu za ansembe ake, amene anakhetsa mwazi wa olungama pakati pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma izi zinachitika chifukwa cha kuchimwa kwa aneneri ake ndi mphulupulu za ansembe ake, amene ankapha anthu osalakwa pakati pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndico cifukwa ca macimo a aneneri ndi mphulupulu za ansembeace, Amene anakhetsa mwazi wa olungama pakati pace.