Lamentations 4:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ankaŵafuulira kuti, “Chokani, inu anthu oipitsidwa. Chokani! Chokani apa! Musakhudzane ndi ife!” Motero adathaŵa, namangoyendayenda, anthu a mitundu ina ankati, “Asadzakhalenso ndi ife.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amafuula kwa iwo, Chokani, osakonzeka inu, chokani, chokani, musakhudze kanthu. Pothawa iwo ndi kusochera, anthu anati mwa amitundu, sadzagoneranso kuno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu akuwafuwulira kuti, “Chokani! Inu anthu odetsedwa!” “Chokani! Chokani! Musatikhudze ife!” Akamathawa ndi kumangoyendayenda, pakati pa anthu a mitundu yonse amati, “Asakhalenso ndi ife.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amapfuula kwa iwo, Cokani, osakonzeka inu, cokani, cokani, musakhudze kanthu. Pothawa iwo ndi kusocera, anthu anati mwa amitundu, Sadzagoneranso kuno.