Lamentations 4:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso athu adatopa nkuyang'anira chithandizo, koma popanda phindu. Tidadikiradikira mtundu wina wa anthu amene sangathe kutipulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maso athu athedwa, tikali ndi moyo, poyembekeza thandizo chabe; kudikira tinadikira mtundu wosatha kupulumutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiponso maso athu atopa nʼkuyangʼana, chithandizo chosabwera nʼkomwe, kuchokera pa nsanja zathu tinadikirira mtundu wa anthu umene sukanatipulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maso athu athedwa, tikali ndi moyo, poyembekeza thandizo cabe; Kudikira tinadikira mtundu wosatha kupulumutsa.