Lamentations 4:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu otilondolawo anali aliŵiro kupambana adembo ouluka mu mlengalenga. Adatipirikitsa ku mapiri, adatilalira ku chipululu kuti atiphe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Otilondola anaposa ziombankhanga za m'mlengalenga m'liwiro lao, anatithamangitsa pamapiri natilalira m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Otilondola akuthamanga kwambiri kuposa ziwombankhanga mu mlengalenga; anatithamangitsa mpaka ku mapiri ndi kutibisalira mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Otilondola anaposa ziombankhanga za m'mlengalenga m'liwilo lao, Anatithamangitsa pamapiri natilalira m'cipululu.