Lamentations 4:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale nkhandwe siziwumira bere, zimayamwitsa ana. Koma anthu anga ndi ankhalwe, ali ngati nthiŵatiŵa zakunkhalango.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Angakhale ankhandwe amapatsa bere, nayamwitsa ana ao; koma mwana wamkazi wa anthu a mtundu wanga wasanduka wankhanza, ngati nthiwatiwa za m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale nkhandwe zimapereka bere kuyamwitsa ana ake, koma anthu anga asanduka ankhanza ngati nthiwatiwa mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Angakhale ankhandwe amapatsa bere, nayamwitsa ana ao; Koma mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga wasanduka wankhanza, ngati nthiwatiwa za m'cipululu.