Lamentations 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Khungu lathu likutentha ngati lili m'ng'anjo chifukwa cha ululu wa njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khungu lathu lapserera ngati pamoto chifukwa cha kuwawa kwa njala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khungu lathu latentha ngati uvuni mʼngʼanjo, chifukwa cha kuwawa kwa njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khungu lathu lapserera ngati pamoto Cifukwa ca kuwawa kwa njala.