Lamentations 5:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ku Ziyoni akazi akuŵachita zadama mwakhakhamizo. M'mizinda ina ya ku Yuda anamwali akuŵachita chimodzimodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anaipitsa akazi m'Ziyoni, ndi anamwali m'midzi ya Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayi agwiriridwa mu Ziyoni, ndi anamwali mʼmizinda ya Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anaipitsa akazi m'Ziyoni, Ndi anamwali m'midzi ya Yuda.