Lamentations 5:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akalonga akuŵapachika pomangirira manja ao, akuluakulu sakuŵalemekeza konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anawapachika akalonga manja ao; sanalemekeze nkhope za akulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akalonga athu akuwapachika pomangirira manja awo, akuluakulu sakuwalemekeza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anawapacika akalonga manja ao; Sanalemekeza nkhope za akulu.