Lamentations 5:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Achinyamata akuŵakakamiza kupera tirigu, anyamata akudzandira nayo mitolo ya nkhuni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anyamata ananyamula mphero, ana nakhumudwa posenza nkhuni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Achinyamata akukakamizidwa kupera tirigu; anyamata akudzandira ndi mitolo ya nkhuni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anyamata ananyamula mphero, Ana nakhumudwa posenza nkhuni.