Lamentations 5:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimwemwe chachoka m'mitima mwathu. Kuvina kwathu kwasanduka kulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chimwemwe cha mtima wathu chalekeka, masewera athu asanduka maliro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimwemwe chachoka mʼmitima yathu; kuvina kwathu kwasanduka maliro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimwemwe ca mtima wathu calekeka, Masewera athu asanduka maliro.