Lamentations 5:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chisoti chathu chaufumu chachoka kumutu, kugwa pansi. Tsoka kwa ife, chifukwa tachimwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Korona wagwa pamutu pathu; kalanga ife! Pakuti tinachimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chipewa chathu chaufumu chagwa pamutu pathu. Tsoka kwa ife, chifukwa tachimwa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Korona wagwa pamutu pathu; Kalanga ife! pakuti tinacimwa.