Lamentations 5:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake mitima yathu yalefuka, chifukwa cha zimenezi m'masomu mwachita chidima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha ichi mtima wathu ufooka, chifukwa cha izi maso athu achita chimbuuzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitima yathu yakomoka chifukwa cha zimenezi, chifukwa cha zinthu zimenezi maso athu sakuona bwino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca ici mtima wathu ufoka, Cifukwa ca izi maso athu acita cimbuuzi;