Lamentations 5:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mwakhala mukutiiŵala nthaŵi yonse? Chifukwa chiyani mwatisiya nthaŵi yaitali chotere?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwanji mutiiwala chiiwalire, ndi kutisiya masiku ambirimbiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani mumatiyiwala nthawi zonse? Chifukwa chiyani mwatitaya nthawi yayitali chotere?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwanji mutiiwala ciiwalire, Ndi kutisiya masiku ambirimbiri;