Lamentations 5:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta mutitembenuzire kwa Inu, kuti tibwerere mwakale. Mutipatsenso masiku onga amakedzana aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutitembenuzire kwa Inu, Yehova, ndipo tidzatembenuzidwadi, mukonzenso masiku athu ngati kale lija.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova mutitembenuzire kwa Inu, kuti tibwerere; mukonzenso masiku athu akhale monga akale,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutitembenuzire kwa Inu, Yehova, ndipo tidzatembenuzidwadi, Mukonzenso masiku athu ngati kale lija.