Lamentations 5:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tili ngati ana amasiye, opanda bambo wao. Amai athu ali ngati akazi amasiye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndife amasiye opanda atate, amai athu akunga akazi amasiye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Takhala amasiye ndi wopanda abambo, amayi athu ali ngati akazi amasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndife amasiye opanda atate, Amai athu akunga akazi amasiye.