Lamentations 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidachita chibwenzi ndi Aejipito ndiponso ndi Aasiriya, kuti mwina iwo nkutipatsako chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tinagwira mwendo Ejipito ndi Asiriya kuti tikhute zakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tinadzipereka kwa Aigupto ndi kwa Asiriya kuti tipeze chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tinagwira mwendo Aigupto Ndi Asuri kuti tikhute zakudya.