Lamentations 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pofunafuna chakudya, timagwa m'zoopsa chifukwa cha anthu opha anzao ku chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Timalowa m'zoopsa potenga zakudya zathu, chifukwa cha lupanga la m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Timapeza chakudya chathu poyika miyoyo yathu pa chiswe chifukwa cha lupanga mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Timalowa m'zoopsya potenga zakudya zathu, Cifukwa ca lupanga la m'cipululu,