Leviticus 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo ansembe aike nthuli za nyamayo, mutu wake pamodzi ndi mafuta omwe, pa nkhuni zimene zili pa guwalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi ana a Aroni, ansembewo, akonze ziwalozo, mutu, ndi mafuta pa nkhuni zili pa moto wa pa guwa la nsembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka ana a Aaroni, wansembe uja, ayike nthuli za nyamayo, mutu wake pamodzi ndi mafuta omwe pa nkhuni zimene zili paguwapo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ana a Aroni, ansembewo, akonze ziwalozo, mutu, ndi mafuta pa nkhuni ziri pa mota wa pa guwa la nsembe;