Leviticus 10:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Mose adafunafuna mbuzi ya nsembe yopepesera machimo, ndipo adapeza kuti adaitentha kale. Ndipo adakalipira Eleazara ndi Itamara, ana a Aroni otsala aja. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yauchimo, ndipo taonani, adaitentha. Ndipo anapsa mtima pa Eleazara ndi Itamara, ana otsalawo a Aroni, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yopepesera machimo koma anapeza kuti anayitentha kale. Apa Mose anakalipira Eliezara ndi Itamara, ana a Aaroni otsala aja nati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yaucimo, ndipo, taonani, adaitentha.