Leviticus 10:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chifukwa chiyani simudadyere pa malo oyera nsembe yopepesera machimo ija? Kodi si yopatulika kwambiri? Kodi siyoperekedwa kwa inu kuti muchotse machimo a mpingo wonse, kuti muŵachitire mwambo wopepesera machimo ao pamaso pa Chauta?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwalekeranji kudya nsembe yauchimo m'malo opatulika, pakuti ndiyo yopatulika kwambiri, ndipo Iye anakupatsani iyo, kuchotsera nayo mphulupulu ya khamulo, kuwachitira chowatetezera pamaso pa Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chifukwa chiyani simunadyere pamalo wopatulika nsembe yopepesera machimo ija? Kodi imene ija siyopatulika? Kodi Yehova sanapereke nyamayo kwa inu kuti muchotse machimo a mpingo wonse powachitira mwambo wa nsembe yopepesera machimo pamaso pa Yehova?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapsa mtima pa Eleazara ndi Itamara, ana otsalawo a Aroni, nati, Mwalekeranji kudya nsembe yaucimo m'malo opatulika, pakuti ndiyo yopatulikitsa, ndipo iye anakupatsani iyo, kucotsera nayo mphulupulu ya khamulo, kuwacitira cowatetezera pamaso pa Yehova?