Leviticus 10:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa magazi ake sadaloŵe nawo m'katikati mwa malo oyera kwambiri, mukadayenera kudyera zimenezi pa malo oyera, monga momwe ndidalamulira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, sanalowe nao mwazi wake m'malo opatulika m'katimo; mukadaidyera ndithu m'malo opatulika, monga ndinakuuzani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti magazi ake sanalowe nawo ku Malo Wopatulika, mukanadya nyama ya mbuziyo pa malo wopatulikawo monga Yehova analamulira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, sanalowa nao mwazi wace m'malo opatulika m'katimo; mukadaidyera ndithu m'malo opatulika, monga ndinakuuzani.