Leviticus 10:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adasenderadi pafupi, naŵanyamula ali ndi mikanjo yao ndi kuŵatulutsira kunja kwa mahema, monga momwe Mose adaŵauzira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anasendera pafupi, nawanyamula osawavula malaya ao a m'kati, kunka nao kunja kwa chigono, monga Mose adauza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anabwera atavala minjiro yawo ndipo anawatenga ndi kuwatulutsa kunja kwa msasawo monga momwe Mose analamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anasendera pafupi, nawanyamula osawabvula maraya ao a m'kati, kumka nao kunja kwa cigono, monga Mose adauza.