Leviticus 11:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nthiŵatiŵa, chipudo, kakoŵa, akabaŵi a mitundu yonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi nthiwatiwa, ndi chipudo, ndi kakowa, ndi kabawi mwa mtundu wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kadzidzi wamphondo, kadzidzi wodzuma, chipudo ndi mtundu uliwonse wa akabawi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi nthiwatiwa, ndi cipudo, ndi kakoa, ndi kabawi mwa mtundu wace;