Leviticus 11:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu akakhudza nyama yofa yokha imene anthu amadya, munthuyo adzakhala woipitsidwa mpaka madzulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ikafa nyama yakudya, iye amene akhudza mtembo wake adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati nyama imene mumaloledwa kudya yafa yokha, ndiye kuti aliyense wokhudza nyama yakufayo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ikafa nyama yakudya, iye amene akhudza mtembo wace adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.