Leviticus 11:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kalulu: ameneyu ndi wonyansa kwa inu, chifukwa ngakhale amabzikula, ziboda zake nzosagaŵikana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kalulu, popeza abzikula koma wosagawanika chiboda, mumuyese wodetsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inanso ndi kalulu, ngakhale amabzikula, zipondero zake nʼzosagawikana. Choncho ndi wodetsedwa, musadye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kalulu, popeza abzikula koma wosagawanika ciboda, mumuyese wodetsedwa.