Leviticus 13:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
limenelo ndi khate lachikhalire limene lili pakhungu pakelo, ndipo wansembe amutchule kuti ndi woipitsidwa. Sikufunika kumtsekera chifukwa ndi woipitsidwadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndilo khate lakale pa khungu la thupi lake, ndipo wansembe amutche wodetsedwa; asambindikiretse popeza ali wodetsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
limenelo ndi khate lachikhalire la pa khungu, ndipo wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Asamutsekere munthu woteroyo pakuti ndi wodetsedwa kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndilo khate lakale pa khungu la thupi lace, ndipo wansembe amuche wodetsedwa; asambindikiritse popeza ali wodetsedwa.