Leviticus 13:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pathupi pake pakaoneka zilonda, ndiye kuti munthuyo ndi woipitsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsiku lililonse ukaoneka pa iye mnofu wofiira, adzakhala wodetsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pa tsiku limene zilonda zidzaoneka pa iye, munthuyo adzakhala wodetsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsiku liri lonse ukaoneka pa iye mnofu wofiira, adzakhala wodetsedwa,