Leviticus 13:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma zilondazo zikasinthikanso ndi kusanduka zoyera, pamenepo munthu wodwalayo abwere kwa wansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena mnofu wofiira ukasandukanso, nusandulika wotuwa, afike kwa wansembe,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma zilondazo zikasinthika ndi kusanduka zoyera, munthuyo ayenera kupita kwa wansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena mnofu wofiira ukasandukanso, nusandulika wotuwa, afike kwa wansembe,