Leviticus 13:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono wansembeyo amuwonetsetse. Zilondazo zikakhala kuti zasanduka zoyera, wansembeyo amutchule munthu wodwalayo kuti ndi wosaipitsidwa. Ndi woyera ameneyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wansembe amuone, ndipo taonani, ngati nthenda yasandulika yotuwa, wansembe amutche woyera wanthendayo; ndiye woyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe amuonetsetse ndipo ngati zilondazo zasanduka zoyera, wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi woyera ndipo adzakhala woyera ndithu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wansembe amuone, ndipo taonani, ngati nthenda yasandulika yotuwa, wansembe amuche woyera wanthendayo; ndiye woyera.