Leviticus 13:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pa khungu la munthu wodwalayo pakakhala chithupsa choti chidapola,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene thupi lili ndi chilonda pakhungu pake, ndipo chapola,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati pa khungu la munthu wodwalayo pali chithupsa chimene chinapola kale,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene thupi liri ndi cironda pakhungu pace, ndipo capola,