Leviticus 13:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe aonetsetse bwino, ndipo chithupsacho chikazama, ubweya wake nusanduka woyera, wansembeyo amutchule munthu wodwala uja kuti ndi woipitsidwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate imene yaphulika pachithupsapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo taonani, ngati chioneka chakumba kubzola khungu, ndipo tsitsi lake lisanduka lotuwa, pamenepo wansembe amutche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate yabuka m'chilondamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe aonetsetse bwino ndipo ngati chikuoneka kuti chazama, ndipo ubweya wa pamalopo wasanduka woyera, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate imene yatuluka mʼchithupsacho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo taonani, ngati cioneka cakumba kubzola khungu, ndipo tsitsi lace lisanduka lotuwa, pamenepo wansembe amuche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate yabuka m'cirondamo.