Leviticus 13:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma wansembe akaonetsetsa, napeza kuti ubweya wake sudasanduke woyera, ndipo chithupsacho sichidazame, koma chikuzimirira, wansembeyo amuike padera wodwalayo masiku asanu ndi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wansembe akachiona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sichinakumba kubzola khungu, koma chazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati wansembe waonetsetsa napeza kuti palibe ubweya woyera ndipo chithupsacho sichinazame, koma chazimirira, wansembeyo amuyike padera wodwalayo kwa masiku asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wansembe akaciona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sicinakumba kubzola khungu, koma cazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;