Leviticus 13:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthendayo ikafalikira pa khungu, wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi woipitsidwa, limenelo ndi khate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ngati chapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa; ndilo khate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati nthendayo ikufalikira pa khungu, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limeneli ndi khate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ngati capitirira khungu, wansembe amuche wodetsedwa; ndilo khate.