Leviticus 13:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma bangalo likakhala pa malo amodzi, osafalikira, chimenecho nchipsera cha chithupsa. Wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi wosaipitsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati chikanga chaima pomwepo, chosakula, ndicho chipsera cha chilonda; ndipo wansembe amutche woyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma bangalo likakhala malo amodzi, wosafalikira, chimenecho ndi chipsera cha chithupsacho, ndipo wansembe alengeze kuti munthuyo ndi woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati cikanga caima pomwepo, cosakula, ndico cipsera ca cironda; ndipo wansembe amuche woyera.