Leviticus 13:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lachisanu ndi chiŵirilo, ngati bangalo lafalikira pa khungu, wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi woipitsidwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wansembe amuone tsiku lachisanu ndi chiwiri; ngati chakula pakhungu, wansembe amutche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri wansembe amuonenso wodwalayo, ndipo ngati bangalo lafalikira pa khungu, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limenelo ndi khate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo wansembe amuone tsiku lacisanu ndi ciwiri; ngati cakula pakhungu, wansembe amuche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate,