Leviticus 13:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwamuna kapena mkazi akakhala ndi nthenda kumutu kapena kundevu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati mwamuna kapena mkazi ali ndi nthenda pamutu kapena pandevu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mwamuna kapena mkazi akakhala ndi nthenda kumutu kapena ku chibwano,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati mwamuna kapena mkazi ali ndi nthenda pamutu kapena pandebvu,