Leviticus 13:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
wodwalayo amete, koma mfunduyo asaimete. Wansembe amtsekere masiku asanu ndi aŵiri ena munthu wodwala mfundu yonyerenyesayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo azimeta, koma osameta pamfundu; ndipo wansembe ambindikiritse iye wamfundu masiku asanu ndi awiri ena;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wodwalayo ametedwe, koma pamene pali mfunduyo pasametedwe. Wansembe amuyike padera munthuyo kwa masiku enanso asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo azimeta, koma osameta pamfundu; ndipo wansembe ambindikiritse iye wamfundu masiku asanu ndi awiri ena;