Leviticus 13:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mfunduyo ikafalikira pa khungu, wodwalayo atayeretsedwa kale,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati mfundu ikula pakhungu atatchedwa woyera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mfundu zonyerenyetsazo zikafalikira pa khungu, wansembe atalengeza kuti ndi woyera,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati mfundu ikula pakhungu atachedwa woyera;