Leviticus 13:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwamuna kapena mkazi akakhala ndi maŵanga oyera pa khungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati mwamuna kapena mkazi ali ndi zikanga pa khungu la thupi lake, zikanga zoyerayera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mwamuna kapena mkazi akakhala ndi mawanga woyera pa khungu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati mwamuna kapena mkazi ali ndi zikanga pa khungu la thupi lace, zikanga zoyerayera;