Leviticus 13:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
wansembe aonetsetse bwino. Maŵanga apakhunguwo akakhala oyerera, ndiye kuti ndi mibuko chabe yotuluka pakhungupo. Tsono munthuyo ndi wosaipitsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wansembe aziona; ndipo taonani ngati zikanga zili pa khungu la thupi lao zikhala zotuwatuwa; ndilo thuza labuka pakhungu; ndiye woyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wansembe aonetsetse mawangawo, ndipo ngati ali otuwa, ndiye kuti ndi mibuko chabe yotuluka pa khungu. Munthuyo ndi woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wansembe aziona; ndipo taonani ngati zikanga ziri pa khungu la thupi lao zikhala zotuwatuwa; ndilo thuza labuka pakhungu; ndiye woyera.