Leviticus 13:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akakhala wopanda tsitsi pa mphumi ndiponso m'litsipa, ndiye kuti ali ndi dazi lapamphumi, koma ndi wosaipitsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati tsitsi lathothoka pamphumi pake ndiye wa masweswe, koma woyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati tsitsi lake layoyoka chapamphumi ndiye kuti ndi dazi la pa chipumi limenelo koma munthuyo ndi woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati tsitsi lathothoka pamphumi pace ndiye wa masweswe, koma woyera.