Leviticus 13:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pa dazi lapankhongo kapena lapamphumi pakakhala banga la nthenda loyera mofiirira, limenelo ndi khate limene likutuluka pa nkhongo kapena pa mphumi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati pali nthenda yotuuluka pakati pa dazi lake la pamutu, kapena la pamphumi, ndipo khate lilikubuka pakati pa dazi lake la pamutu, kapena la pamphumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati pa dazi la pamutu kapena la pa chipumi pakhala chithupsa choyera mofiirira, ndiye kuti ndi khate limenelo lochokera mu dazi la pamutu lija kapena pa chipumi lija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati pali nthenda yotuuluka pakati pa dazi lace la pamutu, kapena la pamphumi, ndipo khate lirikubuka pakati pa dazi lace la pamutu, kapena la pamphumi.