Leviticus 13:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiye kuti munthuyo ndi woipitsidwa ndithu. Wansembe ayenera kumtchula kuti ndi woipitsidwa, ali ndi khate lakumutu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiye wakhate, ndiye wodetsedwa; wansembe amutchetu wodetsedwa; nthenda yake ili pamutu pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiye kuti munthuyo ali ndi khate, motero ndi wodetsedwa. Wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa chifukwa cha chithupsa cha pamutu pakepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiye wakhate, ndiye wodetsedwa; wansembe amuchetu wodetsedwa; nthenda yace iri pamutu pace.