Leviticus 13:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wodwalayo adzakhalabe woipitsidwa nthaŵi zonse pamene ali ndi nthendayo, ndipo akhale payekha kunja kwa mahema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku onse nthenda ikali pa iye azikhala wodetsedwa; ali wodetsedwa, agone pa yekha pokhala pake pakhale kunja kwa chigono.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wodwalayo adzakhala wodetsedwa kwa nthawi yonse imene ali ndi nthendayo. Iye ayenera kumakhala payekha kunja kwa msasa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku onse nthenda ikali pa iye azikhala wodetsedwa; ali wodetsedwa, agone pa yekha pokhala pace pakhale kunja kwa cigono.