Leviticus 13:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
wansembeyo alamule kuti achape chovalacho, ndipo achiike padera masiku asanu ndi aŵiri ena.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo wansembe aziuza kuti atsuke chija pali khate, nachibindikiritse masiku asanu ndi awiri ena;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iye alamulire kuti chinthu choyipitsidwacho achichape. Akatero achiyike padera kwa masiku enanso asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo wansembe aziuza kuti atsuke cija pali khate, nacibindikiritse masiku asanu ndi awiri ena;