Leviticus 13:56 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma wansembe akaonetsetsa napeza kuti nguwiyo njothimbirira atachapa chovalacho, ang'ambe banga la nguwilo pa chovala chathonjecho kapena chachikopacho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wansembe akaona, ndipo taonani, nthenda yazimba ataitsuka, pamenepo aikadzule pa chovala, kapena chikopa, kapena muyaro, kapena mtsendero;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati wansembe aonetsetsa nʼkupeza kuti nguwi ija yathimbirira pa chovala chija kapena pa chinthu chachikopa chija atachichapa, ndiye angʼambeko chinthucho pa banga la nguwiyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wansembe akaona, ndipo taonani, nthenda yazimba ataitsuka, pamenepo aikadzule pa cobvala, kapena cikopa, kapena muyaro, kapena mtsendero;