Leviticus 13:57 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bangalo likaonekanso pa chovalacho kapena pa chinthu chilichonse chopangidwa ndi chikopa, ndiye kuti nguwiyo ikufalikira. Zonse zanguwizo muzitenthe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ikaonekabe pachovala, ngakhale pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pa chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa, ilikubukanso; uchitenthe ndi moto chija chanthenda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati nguwiyo iwonekanso pa chovala chathonje kapena chaubweya ndiye kuti nguwiyo ikufalikira. Chilichonse chimene chili ndi nguwi chiyenera kutenthedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ikaonekabe pacobvala, ngakhale pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pa cinthu ciri conse copangika ndi cikopa, irikubukanso; ucitenthe ndi moto cija canthenda.