Leviticus 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma m'bukowo ukafalikira pa khungu, munthuyo atadziwonetsa kale kwa wansembe kuti amuyeretse, munthuyo akaonekerenso pamaso pa wansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma nkhanambo ikapitirira khungu, atadzionetsa kwa wansembe kuti atchedwe woyera, adzionetsenso kwa wansembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati mʼbukowo ufalikira pakhungu atakadzionetsa kale kwa wansembe ndipo wansembeyo nʼkulengeza kuti munthuyo ndi woyeretsedwa, ndiye kuti apitenso kukadzionetsa kwa wansembeyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma nkhanambo ikapitirira khungu, atadzionetsakwa wansembe kuti achedwe woyera, adzionetsenso kwa wansembe;