Leviticus 13:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe amuwonetsetsenso munthuyo. Akaona kuti m'bukowo wafalikiradi pa khungu, atchule wodwalayo kuti ndi woipitsidwa, limenelo ndi khate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nkhanambo yapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa, ndilo khate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe amuonetsetsenso munthuyo, ndipo ngati mʼbukowo wafalikira pa khungu, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa ndi kuti nthendayo ndi khate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nkhanambo yapitirira khungu, wansembe amuche wodetsedwa, ndilo khate.