Leviticus 13:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu akagwidwa ndi nthenda ya khate, abwere naye kwa wansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene nthenda yakhate ili mwa munthu, azimfikitsa kwa wansembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati munthu aliyense ali ndi nthenda ya pakhungu yoyipitsa thupi, wodwalayo abwere naye kwa wansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene nthenda yakhate iri mwa munthu, azimfikitsa kwa wansembe;